28/08/2026
Zanthu akalakwisa ngati koyenela kupeleka chilango chisakhale chodusa malamulo chifukwa pamawa umazapezeka kuti uli mu mvuto ndiwe mwini wake nkhaniwe pali video imene ikudzungulila masamba achedzo anthu anawauza kuti azipanga zadama pamaso pa ngulu aliyese akuonelela guys ndizochitisa manyazi