30/07/2026
Mkulukuta Block ya Difference Construction 🫡🤭!!!
Wogoba magetsi nyumba amafiyira maso akava kuti nyumba yanuyo munamangira Block ya Difference Construction Ltd😁 nkhani yake amadziwa mmene Block ya Difference imalimbira 😁
Mpanda omangira mkulukuta block wa Difference Construction ngati wagwa mumatola ma block abwino bwino osaphwanyika ili phuli phuli uku ikukuwuzani kuti vuto si ine koma Builder yemwe anamanga mpandawu.
Osayiphonya ngulani anu lero ma block kuchokera ku Difference Construction Ltd
for more information whatsap us
0993 44 12 57