12/08/2026
BWELESANI MA PHONE ANU OMWE AMATHEKA CARD IMODZI NDIPO MUKAIKA CARD INA NETWORK SIBWELESA AYI TISEGULE POGWILISA NTCHITO IMEI NUMBER YANU OR MULI KUTALI
ZIWANIKO IZI.... IMEI ndi nambala yapadera yomwe imazindikiritsa foni yanu pa network. Ndikufotokozereni mwadongosolo motelo i hope mundivesa komaso welengan k*t muziwe zambiri
1. Kodi IMEI ndi chani?
IMEI imatanthauza International Mobile Equipment Identity. Ndi nambala yapadera yomwe imaperekedwa ku mobile device k*ti izindikirike pa ma network.
Nthawi zambiri IMEI imakhala ndi manambala 15. Mwachitsanzo: 356############.
Ngati foni ili Dual SIM(2 sim), nthawi zambiri imakhala ndi IMEI 1 ndi IMEI 2, chifukwa ma SIM awiriwa amagwiritsa ntchito ma network identities osiyana.
2. Nanga IMEI imagwira ntchito yanji?
IMEI imagwiritsidwa ntchito kwambiri pa:
1. Kuzindikiritsa foni pa network — network imatha kudziwa device yomwe ikulumikizana nayo.
2. Kusiyanitsa ma phone — ma phone awiri omwe ndi ofanana atha kukhala ndi ma IMEI osiyana.
3. Kuthandiza pa stolen/lost phone blocking — network/operator angaletse phone yomwe yapezeka k*ti yabedwa kapena yatayika kugwilisa ntchito network
4. Device management — ma network ndi ma service ena angagwiritse ntchito IMEI kuzindikira mtundu wa phone ndi momwe ikugwiritsidwira ntchito.
5. Diagnostics ndi servicing — technician angagwiritse ntchito IMEI pothandiza kuzindikira device inayake komanso kufufuza zambiri za model yake.⁶
*3. Kodi IMEI ndi yofunika motani?*
IMEI ndi yofunika kwambiri pa mobile device, chifukwa ndi imodzi mwa identifiers zazikulu za hardware ya foni.
Ngati IMEI yawonongeka kapena kusowa, foni ingakhale ndi vuto kulumikizana ndi cellular network, ngakhale Wi-Fi ingapitirize kugwira ntchito.
4. Kodi ndingawone bwanji IMEI?
Njira yosavuta ndi kulemba:
* #06 #
kapena kupita ku:
Settings → About Phone → IMEI
Pa ma phone ena IMEI imapezekanso pa bokosi la foni kapena label yake.
5. Chofunika kudziwa kwa technician
IMEI si phone number...