GET a Misili

GET a Misili Handyman and Craft services We make your house a home.

18/09/2026

Nchifukwa chani Cost yopangila install Shower Heater imakhala yokwela kuposa kugula Shower Heater?

01/09/2026

Ndi ufulu wanu wachibadidwe kusamba madzi otentha bwino.
K70,000 Shower Heater yokha.
Tilinawo ku Lilongwe

0999480518

Anachita kutichondelera kuti nafe atiulutsire ma drone
22/08/2026

Anachita kutichondelera kuti nafe atiulutsire ma drone

19/08/2026

Kuvulalira mkati.

Chingakhale chani chapangitsa zimenezi

19/08/2026

Machine abwelera pa duty after a long time

0999480518

Malawi 🇲🇼 colonising
14/08/2026

Malawi 🇲🇼 colonising

Koma uyu alimbetu Sunday lino
13/08/2026

Koma uyu alimbetu Sunday lino

Umisili winawu eeeh 🙌
13/08/2026

Umisili winawu eeeh 🙌

Design iyiyi ya ma cooker 🔥💪Amanena kuti sitingasinthe chilichonse ngati tikupanga zomwezomwezo zomwe zikutilepheletsazo...
13/08/2026

Design iyiyi ya ma cooker 🔥💪

Amanena kuti sitingasinthe chilichonse ngati tikupanga zomwezomwezo zomwe zikutilepheletsazo, omwewo amatinso pawiripawiri sipauzilika.

Mukulephera muli maphunziro koma ngati simkuphunzilamo pano nthawi izakwana muzingomwetulira nkumazifunsa kuti "ndinkaganiza chani ine pamenepaja".

We will scorch🔥 those tapes Basopu
13/08/2026

We will scorch🔥 those tapes
Basopu

Address

Lilongwe

Telephone

+265999480518

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GET a Misili posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to GET a Misili:

Shortcuts

Share