Vinje Green Innovations

Vinje Green Innovations Solar Company

KODI MUKUFUNA KUKHALA AGENT WA VINJE GREEN INNOVATIONS?Zoyenera kuchita;> Lembani kalata yofunsira kukhala Agent >Mukhal...
20/07/2026

KODI MUKUFUNA KUKHALA AGENT WA VINJE GREEN INNOVATIONS?

Zoyenera kuchita;

> Lembani kalata yofunsira kukhala Agent
>Mukhale ndi Smart Phone
>Mukhale ndi MSCE
>National ID (Chithunzi)
>Kalata yakwa mfumu
>Kalata ya guardian /mboni
> Mu kalata mutchule Boma komaso dera limene mukukhala

> tumizani ma form anu ku WhatsApp 0995659859.

Will you be our customer?
03/07/2026

Will you be our customer?

AKASI MULIPO?  za BHO?Ma set a Clean simuwafuna?Zaguleni ma solar otsika mtengo, olimba komanso apamwamba kuno, inu Akas...
19/06/2026

AKASI MULIPO? za BHO?
Ma set a Clean simuwafuna?
Zaguleni ma solar otsika mtengo, olimba komanso apamwamba kuno, inu Akasi๐Ÿ˜๐Ÿ˜
Tili ndi ma solar monga;
โœ… Pico Lanterns
โœ… Solar Home Systems
โœ… Solar Inverters
โœ… Quality Solar Accessories
kaya mzafuna kugula pa CASH kaya pa NGONGOLE, zonse BHO!!!!๐Ÿ‘๐Ÿ‘
Mukagula kwa ife:
โœ” Tizakuikirani ulele (Free Installation)
โœ” Tizakupastsani Warranty ya zaka ziwiri (2 Years Warranty)
Whether you need lighting for your home, power for your business, or a complete solar solution, we are here to help.
๐Ÿ“ž Call or WhatsApp us today: 0995 06 38 68
๐Ÿ“ Visit us at:
Area 47, Sector 3,
Opposite Seventh Day Church,
GHP House, Lilongwe.
Terms & Conditions Apply

AKASI MULIPO?  za BHO?Ma set a Clean simuwafuna?Zaguleni ma solar otsika mtengo, olimba komanso apamwamba kuno, inu Akas...
08/06/2026

AKASI MULIPO? za BHO?

Ma set a Clean simuwafuna?

Zaguleni ma solar otsika mtengo, olimba komanso apamwamba kuno, inu Akasi๐Ÿ˜๐Ÿ˜

Tili ndi ma solar monga;
โœ… Pico Lanterns
โœ… Solar Home Systems
โœ… Solar Inverters
โœ… Quality Solar Accessories

kaya mzafuna kugula pa CASH kaya pa NGONGOLE, zonse BHO!!!!๐Ÿ‘๐Ÿ‘

Mukagula kwa ife:
โœ” Tizakuikirani ulele (Free Installation)
โœ” Tizakupastsani Warranty ya zaka ziwiri (2 Years Warranty)

Whether you need lighting for your home, power for your business, or a complete solar solution, we are here to help.

๐Ÿ“ž Call or WhatsApp us today: 0995 06 38 68

๐Ÿ“ Visit us at:
Area 47, Sector 3,
Opposite Seventh Day Church,
GHP House, Lilongwe.

Terms & Conditions Apply

โ€ŽFriday yafika! โ˜€๏ธโšกโ€Ž B nyamula chikwama uzagule solar kuti nyumba yako izikhala yowala nthawi zonse. ๐Ÿ”‹๐Ÿ’กโ€Žsolar keeps you ...
29/05/2026

โ€ŽFriday yafika! โ˜€๏ธโšก
โ€Ž B nyamula chikwama uzagule solar kuti nyumba yako izikhala yowala nthawi zonse. ๐Ÿ”‹๐Ÿ’ก
โ€Žsolar keeps you going! ๐ŸŒฑ
โ€Ž
โ€Ž
โ€Ž
โ€Ž
โ€Ž

โ€Žโ€ŽMukagula solar kuchokera ku Vinje Green Innovations, kuyika (installation) ndi kwaulere*, simudzalipira ndalama zina z...
27/05/2026

โ€Žโ€ŽMukagula solar kuchokera ku Vinje Green Innovations, kuyika (installation) ndi kwaulere*, simudzalipira ndalama zina zowonjezera.
โ€Ž
โ€ŽSangalalani ndi mphamvu yodalirika komanso yotsika mtengo.
โ€Ž
โ€Ž๐Ÿ“ž Tiyimbireni lero kuti mudziwe zambiri



โ€Ž
โ€Ž

A new week brings new opportunities to grow, innovate, and make a difference. As we begin this week, let's remember that...
25/05/2026

A new week brings new opportunities to grow, innovate, and make a difference. As we begin this week, let's remember that every step toward clean energy is a step toward stronger communities, brighter homes, and a more sustainable future.

Lowani mโ€™gulu la mabanja omwe akusangalala kale ndi magetsi a dzuwa kuchokera ku Vinje Green Innovations.Musatsale mโ€™mbu...
22/05/2026

Lowani mโ€™gulu la mabanja omwe akusangalala kale ndi magetsi a dzuwa kuchokera ku Vinje Green Innovations.
Musatsale mโ€™mbuyo! Bweretsani kuwala odalirika m'nyumba mwanu lero. โ˜€๏ธ๐Ÿ’ก

Kodi mukuvutika ndi nkhawa ya mabilu okwera a magetsi mwezi ndi mwezi? ๐Ÿ˜Ÿ๐Ÿ“ˆ Nthawi yakwana yoti musinthe.Osataya ndalama p...
20/05/2026

Kodi mukuvutika ndi nkhawa ya mabilu okwera a magetsi mwezi ndi mwezi? ๐Ÿ˜Ÿ๐Ÿ“ˆ Nthawi yakwana yoti musinthe.
Osataya ndalama pachabe, sandutsani dzuwa kukhala mphamvu mโ€™nyumba mwanu! โ˜€๏ธโœจ

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vinje Green Innovations posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share